Featured In

Credits

PERFORMING ARTISTS
Mazani
Mazani
Vocals
COMPOSITION & LYRICS
Chifuniro Kasiya
Chifuniro Kasiya
Songwriter
PRODUCTION & ENGINEERING
NEW
NEW
Producer
Ghostly Sounds
Ghostly Sounds
Producer

Lyrics

Kunena zoona ndatopa I don't think I have it in me anymore Kuyesa nde ndayesa nkuthodwa Koma sizikuyenda konse Ndimvelenikoni ndavuka Kuphusha ndikuphusha koma sizikusuntha Kumafuna kulila Misonzi sikutuluka Ambuye ngati mukundinva Ilamuleni Nyanja kuti ichite bata Ngalawa yanga ikumila sinditha kusambila Musalole Kuti namondwe anditenge Namondwe anditenge anditenge Musalole Kuti namondwe anditenge Namondwe anditenge Anditenge Musalole Nyali yanga izime Ndikamagwa mundigwile Ndisamazikaikile ndisazilembele malire Kuthekela ndilanako kokwanilisa Ndikayamba filimu nzimalizisa Chilichonse mmalo mwake mwaikiza Ngati si changa ndizintha kuziwa Sinzikakamiza Musalole Kuti namondwe anditenge Namondwe anditenge anditenge Musalole Kuti namondwe anditenge Namondwe anditenge Anditenge Musalole
Writer(s): Chifuniro Kasiya Lyrics powered by www.musixmatch.com
Get up to 2 months free of Apple Music
instagramSharePathic_arrow_out