Lyrics

Tsararam tsara Saimba Ng'oma, Saimba uuh uuh Saimba ng'oma uh, saimba ng'oma uh Saimba ng'oma, saimba Wakula watha uh, wakula watha uh Wakula watha, wakula Saimba Ng'oma Satsogoza mthenga mavuto akamadza (ooh) Mu mtima kusandusa balaza mu bongo angozaza (ooh ooh) Ekhaekha angodweza mutu wangofasa (wakula wakula) Ekhaekha angolakhula zi nkhawa kusanza (wakula) Limenelo ndiye dziko mwakula (saimba) Limagiligisha limamanga nyakula (saimba) Kaya umapemphela umapanga maula Pena zitenthe ngati uli kunsi kwa mbaula (wakula) Za chinyengo chidule Shatta sungapindule (wakula) Dziko limakuteleka usanaiphule (wakula) Zilimbe kuvala, usamazivule Kumbitsa podzala, asamazizule (wakula) Kukacha kolola (saimba) Suziwa mtima wa moto pakapsa tonola (saimba) Njira yako londola ena osamangolondola Lila mtima uphwe chipite ukangotonthola Chidziwa mchipande powomola Saimba ng'oma uh, saimba ng'oma uh Saimba ng'oma, saimba Wakula watha uh, wakula watha uh Wakula watha, wakula Kulakwisa n'kamodzi kubwelenza nchikhalidwe Uzaphunzira mowawa,anthu amaveka zingwe Uuuh sitibhambatira za ini Ukatalika manja mapeto ake ukayidi Osayedyela m'maso uli ndi chisankho Kusata maloto, kapena zilalako (koma) Kuchita bwino kulibe chidule baba Ofa manja sangayinukhe ataaa Ufulu ndikuyima pa wekha Moni wa munthu osawuka ammati kupempha Udolo ndikukwanisa ndi zomwe uli nazo Timapeza mosiyana simpikisano (No!) Wapambana wapeza chochita Ndalama imadana ndimanja opinda Inde nyengo zako utha kusintha Pali magonizo pamapezekaso njira Saimba ng'oma uh, saimba ng'oma uh Saimba ng'oma, saimba Wakula watha uh, wakula watha uh Wakula watha, wakula
Lyrics powered by www.musixmatch.com
Get up to 2 months free of Apple Music
instagramSharePathic_arrow_out