Lyrics

Yeah yeah yeah (Nyanda made it) Yeah Anamugulira benz Pa birthday akaziyendela Anampezela vephi Sanalore mwanakazi azivutika Koma ukamatha mwezi Siyimalowa mwanakazi achite recharge Mumamuyika dp mwezi onse osamusintha (yeah eh) Koma akati adze malawulo umakuwotcha ndiwe dzulo Anzako akakuyimbira wezulo Unkayesa ngati ndi bodza Akunama yeah eh-eh Utha kumukonda monse momwe ungafune Utha kumupatsa zonse zomwe angafune eh-eh Koma adziwe loyalty is a choice Loyalty is a choice, loyalty is a choice Eya loyalty is a choice Loyalty is a choice, loyalty is a choice yeah Si material things Chikondi chilibe fees Ngati samakukonda sangakhale Olo utamumangira mpanda Uzamupeza ali panja Wekhaso mkuzadabwa Kani zimatere? Koma akati adze malawulo umakuwotcha ndiwe dzulo Anzako akakuyimbira wezulo Iih yeah yeah Utha kumukonda monse momwe ungafune Utha kumupatsa zonse zomwe angafune eh-eh Koma adziwe loyalty is a choice Loyalty is a choice, loyalty is a choice Eya loyalty is a choice Loyalty is a choice, loyalty is a choice yeah Sungamulipire kuti akhulupilike Ngati amafuna, amafuna Amafuna, amafuna adzaonetsa Izi zoti n'namugulira (galimoto) Izi zoti n'nnamuchitira (chilichonse) And you expect loyalty in return Udzalira, udzalira yeah! Utha kumukonda monse momwe ungafune Utha kumupatsa zonse zomwe angafune eh-eh Koma adziwe loyalty is a choice Loyalty is a choice, loyalty is a choice Eya loyalty is a choice Loyalty is a choice, loyalty is a choice yeah Utha kumukonda monse momwe ungafune Utha kumupatsa zonse zomwe angafune eh-eh Koma adziwe loyalty is a choice Loyalty is a choice, loyalty is a choice Eya loyalty is a choice Loyalty is a choice, loyalty is a choice yeah
Lyrics powered by www.musixmatch.com
Get up to 2 months free of Apple Music
instagramSharePathic_arrow_out