Lyrics

Yeyeye yeyeye yeyeyeyeyeye Ndangofika panyumba ndati Ndipume pang'ono nayonso Phone iyo yalira Ndaiyankha ndafunsa Ndindani kodi wandiyankha Kodi mudandifufuta Mwina ndimwangozi pajatu Udangoti zi kundithawa mwa Chipongwe lero ngati malodza Kumvako mawu ako chonde Usandipatse busy M'nakudikira kulira Kuchondelera m'nakudikira su Mkabwera iwe mnakudikira Kulilira Kuchondelera mnakudi Kira sumkabwera ukadangode Khako kundipatsa mtimako M'nakudikira sumkabwera Lero ndazitolera anzako Andi Chengeta m'nakudikira sumka Bwera Achulukirenji anthu padzikopa Aliyense afuna chikondi tsano Mkayambana nanu samakwiye Muzapeza mzanu wachangu Watola zilingati nsima ya Nyama sanyanyala iwe anzako Anjala adzakuliza usamasewere Tse chikondi usamaseweretse Mtima pachoka mzako Pali Malo M'nakudikira kulira Kuchondelera m'nakudikira su Mkabwera iwe mnakudikira Kulilira Kuchondelera mnakudi Kira sumkabwera ukadangode Khako kundipatsa mtimako M'nakudikira sumkabwera Lero ndazitolera anzako Andi Chengeta m'nakudikira sumka Bwera You don't know what you've Got until it's gone until it's Taken away kupatsidwa mtima Mkumauseweretsa mkumaudo Da ngati kampira lero zasoloba Na mwayamba kundisakasaka Saka ukakwera mumtengo Ususatukwane pansi ili ndi Dziko limaseka M'nakudikira kulira Kuchondelera m'nakudikira su Mkabwera iwe mnakudikira Kulilira Kuchondelera mnakudi Kira sumkabwera ukadangode Khako kundipatsa mtimako M'nakudikira sumkabwera Lero ndazitolera anzako andi Chengeta m'nakudikira sumka Bwera
Writer(s): Sam Smack Lyrics powered by www.musixmatch.com
Get up to 2 months free of Apple Music
instagramSharePathic_arrow_out