Top Songs By Lucius Banda
Similar Songs
Credits
PERFORMING ARTISTS
Lucius Banda
Performer
COMPOSITION & LYRICS
Lucius Banda
Composer
Dan Lu
Songwriter
PRODUCTION & ENGINEERING
DJ Ok
Producer
Lyrics
Iwe ndi Ine (iya-na-na-na-yoh)
Yah man (Iwe ndi Ine)
This is ionine soldier Lucius Banda
And the ras in it
Standing shoulder to shoulder
With Dan Lu wachiyawo wangalusa
Atinena sitikhalana
Cholinga chawo tiziyambana
Tisiyane apeze danga
Pachoka nzako pali malo
Ati chikondi chathu sichingalimbe eh
Ndipo sichamuyaya
Mphuno salota Inu wake Ife mpaka kumanda
Onena zinenani
Oseka zisekani
Onyoza zinyozani
Okwiya zikwiyani, ooh yeah
Ife taponda mwala
Ndipo sitikayika ngati pali ena munachedwa
Iwe ndi Ine mpaka kale
Iwe ndi Ine mpaka kale (kavalidwe Iwe mkakusamala)
Iwe ndi Ine (Iye) mpaka kale (poti ndiwe wakunsana)
Iwe ndi Ine mpaka kale
Mumkatilembera malire
Sangathe two months
Kenako yapita five years
Kenako phaa ten years
Takhala limodzi dzaka zonsezi
Akhala akukamba zambirimbiri
Mwakhala mukuponya ma spy in our love life
But here we are
Iye ndi ine eeh, tikasiyane eeh
Chomwe Ambuye adalitsa no man can put a sender
Iye ndi ine eeh, tikasiyane eeh
Chomwe Ambuye adalitsa no man can put a sender
Iwe ndi Ine mpaka kale
Iwe ndi Ine mpaka kale (kavalidwe Iwe mkakusamala)
Iwe ndi Ine (Iye) mpaka kale (poti ndiwe wakunsana)
Iwe ndi Ine mpaka kale
Posiyana pano panatidutsa
Polekana panapitilira
Ndife thupi limodzipalibe chomwe mungachite
Mudzingoyang'ana (Iye ndi Ine) muzingosilira
Potilekanitsa panadutsa we just want nobody
Iwe ndi Ine mpaka kale
Iwe ndi Ine mpaka kale (kavalidwe Iwe mkakusamala)
Iwe ndi Ine (Iye) mpaka kale (poti ndiwe wakunsana)
Iwe ndi Ine mpaka kale (mmh)
Iwe ndi Ine (na-na-na-na) mpaka kale
Iwe ndi Ine mpaka kale (kavalidwe Iwe mkakusamala)
Iwe ndi Ine (Iye) mpaka kale (poti ndiwe wakunsana)
Iwe ndi Ine mpaka kale
Iwe ndi Ine mpaka kale
Iwe ndi Ine mpaka kale
Wayimanya wayimanya
Lyrics powered by www.musixmatch.com