Top Songs By Kell Kay
Credits
COMPOSITION & LYRICS
Kell Kay Kambwiri
Songwriter
Lyrics
You already know
(Tricky Beats, ooh, ooh)
Loved you for a long long time
You've been mine for a long long time
Kwathu unadzawonekeranso
But in my dreams zonsezi
In my dreams
I love you but I can't say
I want you but I can't say
I need you but I can't say
Poti uli ndi wako kale
Wa ndalama kale
Ali ndi chi thilakitale
Komanso ndimawopa ine
Vuto ndine singakwanitse lobola
Vuto ndine singakwanitse lobola
Kandalama kanga ndikochepa
Singakwanitse lobola
Kandalama kanga ndikochepa
Singakwanitse lobola
Is it true what they say?
Mkazi okongola Malawi yonse
Ndimbali zinayi zaku UK
Atinso USA, oh-ah
Anaku controller
Anukugulilanso mortal love
Singakwanitse olo Motorola
Komabe umandidolola
I love you but I can't say
I want you but I can't say
I need you but I can't say
Koma nalota utandilola
Koma lobola inandibalalitsa m'maloto mwanga
Vuto ndine singakwanitse lobola
Vuto ndine singakwanitse lobola
Kandalama kanga ndikochepa
Singakwanitse lobola
Kandalama kanga ndikochepa
Singakwanitse lobola
In my life you comе first like Genesis
My first lovе like a diamond, yeah
I love you but I can't have you
Mthumba mwanga m'mopanda malo
Oh, ndimakukonda koma ndalama ndilibe
Oh, ndimakufila koma singakukwanitse
Vuto ndine singakwanitse lobola
Vuto ndine singakwanitse lobola
Kandalama kanga ndikochepa
Singakwanitse lobola
Kandalama kanga ndikochepa
Singakwanitse lobola
Lyrics powered by www.musixmatch.com