Listen to Wife Material (feat. Pon G) by Phyzix

Wife Material (feat. Pon G)

Phyzix

Hip-Hop/Rap

Lyrics

Sonye Entertainment Kukakhala kunjaku kwacha boo Malawi Music dot com Nyimbo za chimalawi Kukhala kunjaku kwacha boo Ndachita kudzadzamo momomo Wife material tiliyo tiliyo Wife mati ti ti ti Ndinapeza babie anthu adziwe Sindimachibisa sichapadziwe Yemwe zikumuwawa adiwe Komatu ichichi ndi changa chi Lindiwe Sichingadzakupatse patse phindi iwe Chimakhala chili ndi Ine Udzimva iwe Vuto lake iweyo kudzimva iwe Umangogwira akazi openga ma by zweee Zaife ndi zokoma zothira kale Sitimvesana kuwawa tsabola wakale Uyuyu ndi wanga si tempory Ndikanena kuti ndi mugaya si phale Kutetha ngati nali samalani abale Akugungira sugar onyambisisa mbale Mkazi you ngoiwalisa abale Amakomedwesa ngati andale (Very good very good) Mamie ndinu chimkazi chowoneka boo Mumachita kukhala ngat a video Mamie muli pure ngat ka viligo Mukadzafuna banja ife tilipo Ndinu wife material tiliyo tiliyo tiliyo Wife mati ti ti titi Wife material tiliyo tiliyo tiliyo Wife thi thi thithi (Yeee) Ichi ndi chindiwo koma si mpiru Sindinachite kuchiba koma ndi chi deal Ichi ndi chibabe chodzadza fill Dzina lake ndinaliyika kale pa will Chimandikumbusa Mag Maupili Mahope anga aku Primary Ku mphungu Tili mafana oyakhula chizungu She had a chocolate skin ndimamufila khungu Chibabe changachi chanfipatsa khungu Ndikayenda ntaunimu sindiona buthu Ndadwala chikondi 10 pa 10 Chachita kundifika pempeni Ndaonera man ndimalizeni Sindipepha ambuye ndi chilitseni Izizi sizagulu siza mmemo Ineyo ndili mmomo mmenemomo Very good very good Mamie ndinu chimkazi chowoneka boo Mumachita kukhala ngat a video Mamie muli pure ngat ka viligo Mukadzafuna banja ife tilipo Ndinu wife material tiliyo tiliyo tiliyo Wife mati ti ti titi Wife material tiliyo tiliyo tiliyo Wife thi thi thithi Girl you the wife material I just want make you my wife ooo Girl you the one in a million ooo This feeling for you I can't deny ooo Iwe ndiwe mkazi oneka boo Ooneka boo oooneka boo Iwe ndiwe chimkazi chooneka boo Chooneka boo chooneka boo Iwe ndiwe mkazi wofitha boo Wofitha boo wofitha boo Iwe ndi chimkazi chofitja boo Chofitha boo chofitha boo Mamie ndinu chimkazi chowoneka boo Mumachita kukhala ngat a video Mamie muli pure ngat ka viligo Mukadzafuna banja ife tilipo Ndinu wife material tiliyo tiliyo tiliyo Wife mati ti ti titi Wife material tiliyo tiliyo tiliyo Wife thi thi thithi Aaaayaaa Ati Kolokoto Mutu wanga zwee Kolokoto Very good very good Very good very good
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out