Top Songs By Gwamba
Similar Songs
Credits
PERFORMING ARTISTS
Gwamba
Performer
COMPOSITION & LYRICS
Gwamba
Composer
PRODUCTION & ENGINEERING
BFB
Producer
Lyrics
Everytime you're feeling down
Everytime you're feeling weak
Yang'ana kumwamba you'll get there
Everytime you're feeling down
Everytime you're feeling weak
Yang'ana kumwamba you'll get there
You'll get there, you'll get there
Yang'ana kumwamba you'll get there
Yeah, aish
Pena ngati mwina ndingogivah
Ndikupemphera koma mbuye sakundimva
Njala, nthenda, mavuto andiliza
Ndikuwona ngati mwina bible limatinamiza
Zitseko zamadalitso ndayesa ku knocker
Mbuye sakutsegula padakali poloka
Ndikulakwitsa pati? Mwina ndikakwere phiri
Ndiwuzeni zochita, mavutowa ndi ambiri
Mafunso achuluka koma palibe oyankha
Nde m'malo molira timadzukabe nkukankha
Mtima ukuwawa ife timasekelera
Timadziwa tsiku lina madalitso adzatigwera, yes
Everytime you're feeling down
Everytime you're feeling weak
Yang'ana kumwamba you'll get there
Everytime you're feeling down
Everytime you're feeling weak
Yang'ana kumwamba you'll get there
You'll get there, you'll get there
Yang'ana kumwamba you'll get there
Aish, anakupatsa mimba nkuyikana
Usowa chochita poti udakali mwana
Kukanika kugona, usiku kumangolira
Dekha, ambuye Yesu adzakupatsa njira
Unalemba mayenso osakhonza? Lembanso
Kumenya hustle osatheka, menyanso
Osagivah iwe simfana wa weak
Ngati pano sizutheka yesa kumenyanso repeat
Kuli mavuto odetsa nkhawa
Usalire yang'ana za mawa
Everytime you're feeling down
Everytime you're feeling weak
Yang'ana kumwamba you'll get there
Everytime you're feeling down
Everytime you're feeling weak
Yang'ana kumwamba you'll get there
You'll get there, you'll get there
Yang'ana kumwamba you'll get there
Everytime you're feeling down
Everytime you're feeling weak
Yang'ana kumwamba you'll get there
Everytime you're feeling down
Everytime you're feeling weak
Yang'ana kumwamba you'll get there
You'll get there, you'll get there
Yang'ana kumwamba you'll get there
You'll get there, you'll get there
Yang'ana kumwamba you'll get there
Lyrics powered by www.musixmatch.com