Lyrics

Ooh oooh! oh oh Ndiuze! Kuyambira pomwe ndakuona Mtima wanga sumakhala pansi Ukaphoda mama ukathinitsa slit kusawutsa unyamata wanga Ndikaganiza salary yanga Zosowa zako sindingakwanitse Ukamadutsa ndimangopenya Window shopping, kukusilira Tsiku lina udandipatsa chanza Nkono wako utawulowolora Tsiku lina udandisekelera Za chikondi iwe pa ine umakayika Kumayesa woku waver wina Amene anali kumbuyo kwanga Osadziwa umkandifuna Koma poti mkazi sukanayankhura Kuopa kuwoneka desperate Koma sign yokha ukanandipatsa ooh oh Ukanangophinya diso Ukanangondinong'oneza iwe Ukandikanga m'manja Sindimkadziwa umandifuna Amayi, musaope mkazi akatchena Kutchenaku, ndimafuna inu mundikonde Tingakongole bwanji Tichisowa chikondi chabambo Tingalemere bwanji Sindingagule chikondi Mai wawe ay ay ay ay oh Mai wawe ay ay ay ay oh Masiku ano zinthu zinasintha Ndikale lomwe akazi anali pansi Akazi ena lero ndizikhwaya Zikuyendera range rover sport Kukamuwona panyumba pake Chilichonse ndicha England Akasamba zodzoladzola Iwe kugulitsa kugula ka vitz Ungayambile pati kufusira? Poti kenako ufusira ntchito Sungadziwe ngati angakulore Poyang'anira kulemera kwake Umuyang'ane maso kwambiri Udzawona misozi ya usiwa Chomwe asowa ndi chikondi Ngati wakukonda usaope nena Sudziwa naye amakufuna Koma monga mkazi sangayankhure ooh oh Ukanangophinya diso Ukanangondinong'oneza iwe Ukandikanga m'manja Sindimkadziwa umandifuna Amayi, musaope mkazi akatchena Kutchenaku, ndimafuna inu mundikonde Tingakongole bwanji Tichisowa chikondi chabambo Tingalemere bwanji Sindingagule chikondi Mai wawe ay ay ay ay oh Mai wawe ay ay ay ay oh Mami-ma mami-ma U-la-la-la ooh ooh ooh! Whoa whoa! (Ukanangophinya diso) Ukanangophinya diso (ooh) Ukanangondinong'oneza (nong'oneza weh) Ukanandikanda m'manja (ooh) Sindimkadziwa umandifuna (Amayi)
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out